Zatsopano pa JW.ORG

2024-05-01

NSANJA YA OLONDA

Kodi Tingapeze Kuti Malangizo Otithandiza Kusankha Zinthu Mwanzeru?

Phunzirani mmene mungasankhire zinthu mwanzeru zomwe zingadzathandize inuyo ndi banja lanu.

2024-05-01

NKHANI ZINA

Kuteteza Akazi—Zimene Baibulo Limanena

Mulungu amaona kuti akazi ayenera kutetezedwa. Onani chifukwa chake amaona choncho komanso zimene adzachite pothetsa nkhanza zonse zimene anthu amachitira akazi.

2024-04-23

KHALANI MASO

Kodi Anthu Adzasiya Liti Kumenya Nkhondo?​—Zimene Baibulo Limanena

Posachedwapa nkhondo zonse zidzathetsedwa. Baibulo limafotokoza mmene zimenezi zidzachitikire.

2024-04-23

NKHANI ZINA

Kodi Choonadi Ndi Chofunikabe Masiku Ano?

Baibulo lingakuthandizeni kudziwa choonadi m’dziko lomwe anthu ambiri akumafalitsa mabodza.

2024-04-16

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Muziphunzira Mwakhama Kuti Mukhale Maso

2024-04-16

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Mafunso Ochokera kwa Owerenga​​—⁠July 2024

Kodi “mkazi” wotchulidwa pa Yesaya 60:1 ndi ndani, nanga ‘anaimirira’ bwanji komanso anaonetsa bwanji “kuwala”?

2024-04-16

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Kodi Mungatani Kuti Muzolowere Mukasamukira Mumpingo Wina?

Akhristu ambiri zimawayendera bwino akasamukira mumpingo watsopano. Kodi n’chiyani chingakuthandizeni ngati mwasamukira mumpingo wina? Onani mfundo 4 zimene zingakuthandizeni kuti muzolowere msanga mpingo watsopanowo.

2024-04-16

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

July 2024

M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira September 9–​October 6, 2024.

2024-04-15

NYIMBO ZA BROADCASTING

“Uthenga Wabwino” (Nyimbo ya Msonkhano wa 2024)

Kuyambira kale mpaka pano, anthu akhala akulalikira za uthenga wabwino mosangalala. Ntchitoyi ndi yaikulu kwambiri. Yesu ndi amene amaitsogolera ndipo angelo amathandiza nawo pa ntchitoyi.

2024-04-12

NKHANI ZINA

Muzithandiza Ena Kuti Musamasungulumwe​—Kodi Baibulo Limati Chiyani?

Onani njira ziwiri zimene mungachite kuti mupindule pothandiza anthu ena.