Pitani ku nkhani yake

Zokhudza Mboni za Yehova Padziko Lonse

  • Mayiko amene a Mboni za Yehova amalambira Mulungu​—239

  • Mboni za Yehova padziko lonse​—8,816,562

  • Maphunziro a Baibulo aulere​—7,281,212

  • Anthu amene anapezeka pa mwambo wokumbukira imfa ya Yesu Khristu​—20,461,767

  • Mipingo​—118,177

 

Mboni za Yehova Padziko Lonse

Timapezeka padziko lonse ndipo timachokera m’mitundu komanso zikhalidwe zosiyanasiyana. Mwina mukudziwa kuti timagwira ntchito yolalikira koma timagwiranso ntchito zina zothandiza anthu a m’madera athu.

Onaninso

MABUKU

Lipoti la Chaka cha Utumiki cha 2023 la Mboni za Yehova Padziko Lonse

Onani zimene a Mboni za Yehova achita pa ntchito yolalikira padziko lonse kuyambira mu September 2022 mpaka August 2023.

NSANJA YA OLONDA

Kodi a Mboni za Yehova Mumawadziwa Bwinobwino?

Kodi inuyo mumaona a Mboni ngati mmene anthu ena omwe atchulidwa m’nkhaniyi amaganizira?