Onani zimene zilipo

Yehova Anapitilizabe Kuonetsa Kukoma Mtima Kosatha

Onani mmene Yosefe anaonetsela kuti anali kukonda Mulungu ndi anthu ena, ngakhale kuti anali na mavuto ambili. Komanso mmene anaonela cikondi ca Yehova pa iye m’mayeselo ake onse. Yatengedwa pa Genesis 37:1-36; 39:1-47:12.