Pulogilamu ya 2018 ya Msonkhano Wacigawo

Pulogilamu ya 2018 ya Msonkhano Wacigawo wa Mboni za Yehova wa mutu wakuti, ‘Khalani Olimba Mtima’!

Tsiku Loyamba

Pulogilamu ya tsiku limeneli lazikidwa pa lemba la Yoswa 1:7 limene limati, ‘Khalani wolimba mtima kwambili.’

Tsiku Laciŵili

Tingalankhule bwanji mau a Mulungu mopanda mantha?

Tsiku Lacitatu

Zocitika zam’tsogolo zidzafuna kuti atumiki a Mulungu akhale olimba Mtima.

Mau kwa Osonkhana

Dziŵani zambili zokhudza msonkhano wacigawo.