Pulogilamu ya Msonkhano Wacigawo wa mu 2019

Pulogilamu ya Msonkhano Wacigawo wa mu 2019 wa Mutu Wakuti “Cikondi Sicitha”!.

Tsiku Loyamba

Pulogilamu ya tsiku loyamba yazikidwa pa 1 Atesalonika 4:9—“Mulungu Amakuphunzitsani Kukondana.”

Tsiku Laciŵili

Pulogilamu ya tsiku laciŵili yazikidwa pa Aefeso 5:2—“Yendanibe M’cikondi.”

Tsiku Lacitatu

Pulogilamu ya tsiku lacitatu yazikidwa pa Yuda 21—“Pitilizani kucita zinthu zimene zingacititse Mulungu kukukondani.”

Mawu kwa Osonkhana

Mawu othandiza kwa opezeka pa msonkhano wacigawo wa Mboni za Yehova.