GALAMUKA! Na. 1 2020 | Pezani Thandizo pa Nkhawa Zanu

Anthu ambili amavutika na nkhawa. Komabe, pali zambili zimene mungacite kuti mupeze thandizo lofunikila.

Kodi Muli na Nkhawa?

Pali zambili zimene mungacite kuti nkhawa zisakupanikizeni kwambili.

Kodi N’zinthu Ziti Zimabweletsa Nkhawa?

Onani zina mwa zinthu zimene zimabweletsa nkhawa, na kuona ngati pali zimene zikukhudzani.

Kodi Nkhawa N’ciani?

Nkhawa ni mbali ya umoyo wathu. Onani mmene nkhawa yaikulu ingakhudzile thupi lanu.

Zimene Mungacite kuti Muthane na Nkhawa

Onani zina mwa mfundo zothandiza zimene zingakuthandizeni kucepetsa kapena kuthana na nkhawa.

N’zotheka Kukhala na Umoyo Wopanda Nkhawa

Pa ife tekha sitingakwanitse kuthetsa zinthu zonse zimene zimatibweletsela nkhawa mu umoyo wathu. Koma Yehova angakwanitse.

“Mtima Wodekha Ndiwo Moyo wa Munthu”

Mawu amenewa opezeka pa Miyambo 14:30, amaonetsa kuti malangizo a m’Baibo ni othandiza nthawi zonse.