Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Kodi Mungakonde Kudziŵa Zambili?

Kodi Mungakonde Kudziŵa Zambili?

Munthu wina wanzelu analemba kuti: “Nzelu ndiyo cinthu cofunika kwambili. Peza nzelu, ndipo pa zinthu zonse zimene upeze, upezenso luso lomvetsa zinthu.” (Miyambo 4:7) Mlengi wathu amatiphunzitsa kuti tikhale anzelu komanso omvetsa zinthu n’colinga cakuti tizipanga zisankho zabwino na kukhala na umoyo wacimwemwe.

Kuti mudziŵe zambili zokhudza malangizo anzelu a m’Baibo, pitani pa jw.org. Pamenepo mudzapeza . . .

  • BAIBO

  • MAVIDIYO

  • MAVIDIYO A TUKADOLI

  • MBALI ZA KUFUNSA MAFUNSO

  • NKHANI

Zonsezi ni zaulele, ndipo zimathandiza anthu a misinkhu yosiyana-siyana komanso a zikhalidwe zosiyana-siyana.