Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Tingatsimikizile Bwanji Kuti Baibulo Limakamba Zoona?

Tingatsimikizile Bwanji Kuti Baibulo Limakamba Zoona?

Baibulo imakamba yokha kuti ni “Mau a Mulungu,” “amene sanganame.” (1 Atesalonika 2:​13; Tito 1:2) Kodi Baibulo imakamba zoona kapena ni buku la nthano cabe?