Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Kodi Kumwamba na Dziko Lapansi Zinacita Kulengedwa?

Kodi Kumwamba na Dziko Lapansi Zinacita Kulengedwa?

Thambo, kuphatikizapo dziko lapansi, n’lalikulu kwambili komanso n’locititsa cidwi. Kodi zinthu zonsezi zinakhalako bwanji? Kodi zimene Baibo imakamba ponena za ciyambi ca cilengedwe n’zoona?