Onani zimene zilipo

Phunzilo 12: Kalebe na Sofiya Apita ku Beteli

Phunzilo 12: Kalebe na Sofiya Apita ku Beteli

Ni zinthu zokondweletsa ziti zimene Kalebe na Sofiya anaona pamene anapita ku Beteli? Nanga iwe ufuna kukaona ciani ukabwela ku Beteli?

 

Mungakondenso Izi

ZIMENE BAIBO IMAPHUNZITSA

Zocita za Ana

Seŵenzetsani zocita zosangalatsazi, zozikika pa Baibo, pophunzitsa ana makhalidwe auzimu.