Phunzilo 14: Konzekela Yankho Lako
N’cifukwa ciani kukonzekela kukayankhapo pa misonkhano n’kofunika kwambili? Nanga ungakonzekele bwanji?
Mungakondenso Izi
ZIMENE BAIBO IMAPHUNZITSA
Zocita za Ana
Seŵenzetsani zocita zosangalatsazi, zozikika pa Baibo, pophunzitsa ana makhalidwe auzimu.