Mboni za Yehova Padziko Lonse

Armenia

Mfundo Zachidule—Armenia

  • 3,103,000—Chiwerengero cha anthu
  • 11,313—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 134—Mipingo
  • Pa anthu 277 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NKHANI

Boma la Armenia Lazindikira Kuti Anthu Okana Usilikali Ali Ndi Ufulu

Zimene Khoti Loona za Ufulu wa Anthu ku Europe lakhala likugamula, zathandiza kwambiri dziko la Armenia pa nkhani yopereka ntchito zina kwa anthu okana usilikali ndipo panopa zinthu zikuyenda bwino.

NKHANI

Gulu Loyamba la Mboni za Yehova ku Armenia Lamaliza Kugwira Ntchito Zimene Linapatsidwa Litakana Kulowa Usilikali

Panopo a Mboni ku Armenia angathe kugwira ntchito zimene sizikusemphana ndi zomwe amakhulupirira ndipo ntchitozo zimathandiza anthu ambiri.

NKHANI

Dziko la Armenia Latulutsa M’ndende Anthu Amene Anamangidwa Chifukwa Chokana Kulowa Usilikali

Kodi chinachitika n’chiyani pa mlandu wokhudza kumangidwa kwa anthu a Mboni za Yehova mpaka kutulutsidwa kwawo m’ndende?