Mboni za Yehova Padziko Lonse

Austria

  • Dera lotchedwa Hallstatt ku Austria​—Akulalikira nyumba ndi nyumba

  • Vienna, Austria—Akulalikira ku Michaelerplatz

  • Dera lotchedwa Hallstatt ku Austria​—Akulalikira nyumba ndi nyumba

  • Vienna, Austria—Akulalikira ku Michaelerplatz

Mfundo Zachidule—Austria

  • 9,105,000—Chiwerengero cha anthu
  • 22,443—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 283—Mipingo
  • Pa anthu 411 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

Akuluakulu a Tauni Ina ku Austria Anachita Mwambo Wokumbukira a Mboni 31 Omwe Anazunzidwa Komanso Kuphedwa mu Ulamuliro wa Chipani cha Nazi

Chikwangwani cha ku Techelsberg chinakonzedwa pokumbukira a Mboni za Yehova omwe anazunzidwa ndi a chipani cha Nazi pa nthawi ya Nkhondo Yachiwiri ya Padziko Lonse.

KUTHANDIZA ENA

Kuthandiza Anthu Othawa Kwawo Omwe Ali ku Central Europe

Anthu othawa kwawo amafunikanso kuwalimbikitsa osati kungowapatsa chakudya ndi malo okhala basi. A Mboni ongodzipereka akulimbikitsa anthu ndi uthenga wa m’Baibulo komanso kuwathandiza kukhala ndi chiyembekezo.

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Bambo Anga Anamwalira Koma Ndinapeza Bambo Ena

Werengani mbiri ya moyo wa M’bale Gerrit Lösch, wa m’Bungwe Lolamulira.

A Mboni za Yehova Analandira Ulemu Pamwambo Wokumbukira Anthu Amene Anazunzidwa M’ndende ya Gusen

Pa April 13, 2014, Anaika chipilala chokumbukira anthu 450 Mboni amene anamangidwa ndi chipani cha Nazi m’ndende ya Mauthausen ndi Gusen ku Austria.