Mboni za Yehova Padziko Lonse

Central African Republic

Mfundo Zachidule—Central African Republic

  • 5,119,000—Chiwerengero cha anthu
  • 2,932—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 64—Mipingo
  • Pa anthu 1,791 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Ndayesetsa Kuti Ndisagwe Ulesi

Nkhaniyi ikufotokoza zinthu zosangalatsa zimene Maxim Danyleyko wakumana nazo pa zaka 68 zimene wakhala akuchita umishonale.