Mboni za Yehova Padziko Lonse

Côte d'Ivoire

  • Abidjan, Côte d’Ivoire​—Kugawira kabuku ka Mverani Mulungu

Mfundo Zachidule—Côte d'Ivoire

  • 29,389,000—Chiwerengero cha anthu
  • 12,712—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 227—Mipingo
  • Pa anthu 2,436 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Anadzipereka ndi Mtima Wonse

Alongo ambiri amene anasamukira kumayiko ena poyamba ankadzikayikira. Kodi anatani kuti alimbe mtima? Kodi aphunzirapo chiyani atatumikira kudziko lina?