Mboni za Yehova Padziko Lonse

Cambodia

Mfundo Zachidule—Cambodia

  • 16,855,000—Chiwerengero cha anthu
  • 1,116—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 17—Mipingo
  • Pa anthu 15,295 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

GALAMUKANI!

Dziko la Cambodia

N’chifukwa chiyani anthu oti angokumana koyamba amatchulana kuti achimwene, chemwali, azakhali, amalume kapena agogo?

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Zimene Ndinasankha Ndili Mwana

Mnyamata wina wa ku Columbus, Ohio, U.S.A. anaganiza zophunzira Chikambodiya. N’chifukwa chiyani anachita zimenezi? Kodi zimenezi zinakhudza bwanji zimene anadzachita m’tsogolo?