Mboni za Yehova Padziko Lonse

Liberia

  • Pafupi ndi Monrovia, ku Liberia​—Akugawira kapepala kakuti Moyo m’Dziko Latsopano la Mtendere

Mfundo Zachidule—Liberia

  • 5,432,000—Chiwerengero cha anthu
  • 7,922—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 146—Mipingo
  • Pa anthu 745 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi