Mboni za Yehova Padziko Lonse

Taiwan

  • Taichung, Taiwan—Akugawira kapepala kofotokoza nkhani za m’Baibulo kwa munthu amene akugula zinthu kumsika wotchedwa Yizhong Night

Mfundo Zachidule—Taiwan

  • 23,375,000—Chiwerengero cha anthu
  • 11,460—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 177—Mipingo
  • Pa anthu 2,060 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NKHANI

Pulogalamu Yopereka Ntchito zina Kwa Anthu Okana Usilikali ku Taiwan Ikuyenda Bwino Kwambiri

Boma la Taiwan linapereka mwayi wogwira ntchito zina za boma kwa anthu okana usilikali.

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Anadzipereka ndi Mtima Wonse ku Taiwan

A Mboni za Yehova oposa 100 apita kukatumikira ku Taiwan. Onani mmene zinthu zikuyendera pa moyo wawo komanso zimene zikuwathandiza kutumikira bwino.