Pitani ku nkhani yake

Umboni Wasayansi Wosonyeza Kuti Baibulo Ndi Lolondola

Kodi Tingadziwe Bwanji Kuti Baibulo Limanena Zoona?

Ngati Baibulo linachokeradi kwa Mulungu, ndiye kuti liyenera kukhala losiyana kwambiri ndi mabuku ena onse.

Kodi Sayansi Imagwirizana ndi Baibulo?

Kodi m’Baibulo muli mfundo zolakwika zokhudza sayansi?

Kodi Mulungu Anayamba Liti Kulenga Zinthu?

Yankho lake lagona pa mmene mawu akuti “pachiyambi” ndiponso “tsiku” anawagwiritsira ntchito m’buku la Genesis.

Kodi Ndi Lachikale Kapena Limanena Zinthu Zoti Ena Sanazitulukire?

Baibulo si buku la sayansi koma mungadabwe ndi zimene limanena pa nkhani za sayansi.

Kodi Sayansi Imatithandiza Bwanji?

Ndi mfundo iti ya sayansi yomwe imawachititsa kutsutsa zoti kuli Mulungu?

Ignaz Semmelweis

Mabanja onse akuyenera kumuthokoza kwambiri munthu ameneyu. Chifukwa chiyani?

Tione Zakale—Galileo

Mu 1992, Papa Yohane Paulo Wachiwiri anavomereza kuti tchalitchi cha Katolika chinalakwitsa kuimba Galileo mlandu chifukwa cha ntchito yake.

Aristotle

Matchalitchi anayamba kuphunzitsa zimene Aristotle ankakhulupirira.

Mulungu Anapereka Mfundo Zokhudza Ukhondo Asayansi Asanazitulukire

Aisiraeli zinthu zinkawayendera bwino chifukwa chotsatira malangizo a Mulungu okhudza ukhondo.