NSANJA YA MLONDA March 2015 | Mungacite Ciani Kuti Muzisangalala ndi Nchito Yanu?

Anthu ambili amasangalala ndi nchito yao ndipo amaona kuti imawapindulitsa kwambili. N’ciani cawathandiza kuti azisangalala ndi nchito yao?

NKHANI YA PACIKUTO

Kodi Kugwila Nchito Mwamphamvu N’kofunikadi?

Anthu ena amaona kuti kugwila nchito yamanja kumawacotsela ulemu. Koma pali anthu ambili amene amasangalala ndi nchito yao. N’ciani cinawathandiza kukhala ndi maganizo oyenela pa nchito yao?

NKHANI YA PACIKUTO

Mungacite Ciani Kuti Muzisangalala Ngati Mumagwila Nchito Yolimba?

Onani malangizo ena a m’Baibulo amene angakuthandizeni kukhala wosangalala ndi wokhutila ndi nchito yanu.

KUKAMBILANA NDI MUNTHU WINA

N’cifukwa Ciani Tifunika Kuphunzila Baibulo?

Ngakhale kuti Baibulo linalembedwa kale kwambili, mfundo zake ndi zothandiza masiku ano. Kodi mfundo za m’Baibulo zingakuthandizeni bwanji pa umoyo wanu?

BAIBO IMASINTHA ANTHU

Ndinasangalala Ndi Mayankho Omveka Bwino a m’Baibulo

A Ernest Loedi anapeza mayankho a mafunso ofunika kwambili okhudza umoyo. Mayankho omveka bwino a m’Baibulo anawathandiza kukhala ndi ciyembekezo codalilika.

TENGELANI CIKHULUPILILO CAWO

“Kodi Mulungu Sindiye Amamasulila Maloto?”

N’ciani cinathandiza Yosefe kumasulila molimba mtima maloto a mkulu wopelekela cikho wa ku Iguputo, mkulu wa ophika mkate, ndi a Farao? Zinatheka bwanji kuti Yosefe acoke m’ndende ndi kukakhala m’nyumba ya mfumu pa tsiku limodzi cabe?

Kuyankha Mafunso a m’Baibulo

Ganizilani mtendele ndi citetezo zimene boma la padziko lonse lingabweletse. N’cifukwa ciani tiyenela kukhulupilila lonjezo la Mulungu lakuti adzabweletsa boma labwino? Ndani angakhale wolamulila wabwino wa boma limenelo?