Mboni za Yehova Padziko Lonse

French Guiana

Mfundo Zachidule—French Guiana

  • 312,000—Chiwerengero cha anthu
  • 2,937—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 46—Mipingo
  • Pa anthu 109 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

ZOCHITIKA PA MOYO

Ulendo Wokalalikira kwa Anthu Okhala M’mphepete mwa Mtsinje wa Maroni

A Mboni za Yehova 13 akunyamuka pa ulendo wokalalikira uthenga wa m’Baibulo wopatsa chiyembekezo kwa anthu okhala m’madera akutali m’nkhalango ya Amazon ku South America.