Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Tikuthokoza

Tikuthokoza

Pangani Dawunilodi:

  1. 1. Ndikavutika

    Ndikuda nkhawa,

    Mumandimva.

    Ndikuthokoza.

  2. 2. Kaya mavuto,

    Angakulenso,

    Mumayankha,

    Tikuthokoza.

  3. 3. Tisadere nkhawa pa chilichonse.

    Mudzatiteteza

    Tikakhulupirira kuti inu

  4. 4. Mudzatithandiza

    Pomwe zavuta.

    Muli nafe,

    Tikuthokoza.

  5. 5. Mumakonda okukondani.

    Muli nafe, tikuthokoza.